Some photos showing my house, relations and my church in Blantyre, Malawi.
posted by Joe Mlenga @ 1:18 pm
your photo on the verandah,munakwinya nkhopetu! munalusanji?
Zimene ndimafuna that day sizimapezeka
powelenga news paper po za fake basi! amawelenga nyuzi mu sunlight yambili choncho? simunapange science ku pulaimale?????
Ndinkamva kuzizila Saturday mmawa, so ndimaothera dzuwa with nyuzipepa against dzuwa kuti maso asafe!
Post a Comment
<< Home
Malawian with a wide of range of interests including human rights, journalism, ICT, sport, Christian activities etc
View my complete profile
4 Comments: